JEG Tellem - PeNAPaKe (feat. Malinga)

Cuff B productions tElLeM
Yeye
Ya achina
Yahman yah
Fully
Hello hie hawayu
Paja man munati ndihalle chama two
Nde ndikuona kunja
Ndikuthayima DZUWA Ndangotino mhhu ndisakhalebe pa cool
Anyway yo nkhani nja simple
Dollar ija tinali nayo kantchito
Nafeso mwina Ititumikileko
Patown PANO tiphushileko hustle
Nde ngati nkotheka
Mungoponya ku phone poti njochepa
Tisachite kufika mpaka popempha
Enafe ndaphuma ndama short temper
Nde eh
Ase ndikudikila penapake
Ikadyela ndikuona kenakake
Pa easy tu NDIKUTCHULA
Kwatsala two games tikiti tiyiphula
Nanenso akundikwenya ena Ake
Ndinatenga mponda kwa winawake
Ma phone simukuyankha tibwera konko mutisungitse Chinachake
Mmhuu ayi sindine ozemba
Ndikukumbukila
Ndinanena lolemba
Utcheke message zomwe ndinalemba
Ndinafotokoza Ndiposo ndimapempha
Noh
Mpakana mwatenga chi ngemba
Kuyamba kundikwenya
zowona ma memba
Koma
Kunditsatila mpaka ku mpemba
Munditengetu bwino nane ndimapenga
Ah ah Inu a jossen
Ngati pali mangawa nde achotseni
Ndi Bale wanu ine ngakunyozeni?
Mwawawuza a Mikozi tamuposteni
Asah
Ase ndikudikila penapake
Ikadyela ndikuona kenakake
Pa easy tu NDIKUTCHULA
Kwatsala two games tikiti tiyiphula
Nanenso akundikwenya ena Ake
Ndinatenga mponda kwa winawake
Ma phone simukuyankha tibwera konko mutisungitse Chinachake
Ndipatse zanga
Mphwanga
Moyo siophweka
Ndiku gagada da
Bwoy you are go dead
Where my money at
Where my money dey
Where my money at
Cheddar
Ase ndikudikila penapake
Ikadyela ndikuona kenakake
Pa easy tu NDIKUTCHULA
Kwatsala two games tikiti tiyiphula
Nanenso akundikwenya ena Ake
Ndinatenga mponda kwa winawake
Ma phone simukuyankha tibwera konko mutisungitse Chinachake
Ase ndikudikila penapake
Ikadyela ndikuona kenakake
Pa easy tu NDIKUTCHULA
Kwatsala two games tikiti tiyiphula
Nanenso akundikwenya ena Ake
Ndinatenga mponda kwa winawake
Ma phone simukuyankha tibwera konko mutisungitse Chinachake
Fully


Written by:
Malinga Mafia, JOY Gondwe

Publisher:
Lyrics © O/B/O DistroKid

Lyrics powered by Lyric Find

JEG Tellem

View Profile